Be Humble

Let me tell you why I'm not khamani khamani with music

Ena oyimbawa ndi osakhalitsa pamene ine i don't just do music because i myself I'm music

Look at oyimba enawa they started zinthu zoti sangazapitilize unless asinthe the story ...ine sindikuthamangila kulikonse mine are prophetic songs

Leave your comment