Zachikondi

Ndikanakondwa kukhala mchikondi,
Koma zikundiopsya zinatengera ada ena ake kudothi,
Ndinangosankha music kugwa nayo mchikondi,
Kuti mwina ndizakhala hot

Leave your comment